Yoswa 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa atanyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo. Pa tsiku la 7 mudzagube kuzungulira mzindawo maulendo 7, ansembewo akuliza malipenga.+ Yoswa 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa ulendo wa 7 wozungulira mzindawo, ansembe aja analiza malipenga awo, ndipo Yoswa anauza asilikaliwo kuti: “Fuulani!+ Pakuti Yehova wakupatsani mzindawu.+
4 Ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa atanyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo. Pa tsiku la 7 mudzagube kuzungulira mzindawo maulendo 7, ansembewo akuliza malipenga.+
16 Pa ulendo wa 7 wozungulira mzindawo, ansembe aja analiza malipenga awo, ndipo Yoswa anauza asilikaliwo kuti: “Fuulani!+ Pakuti Yehova wakupatsani mzindawu.+