Deuteronomo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tamverani Aisiraeli inu, lero mukuwoloka Yorodano+ kulowa m’dziko limene mukukalilanda kwa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inuyo.+ Mukukalanda mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Yoswa 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mzinda wa Yeriko unatsekedwa mwamphamvu chifukwa cha ana a Isiraeli. Palibe amene anali kutuluka kapena kulowa mumzindawo.+
9 “Tamverani Aisiraeli inu, lero mukuwoloka Yorodano+ kulowa m’dziko limene mukukalilanda kwa mitundu ikuluikulu ndi yamphamvu kuposa inuyo.+ Mukukalanda mizinda ikuluikulu yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+
6 Mzinda wa Yeriko unatsekedwa mwamphamvu chifukwa cha ana a Isiraeli. Palibe amene anali kutuluka kapena kulowa mumzindawo.+