1 Samueli 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamapeto pake, Sauli anauza atumiki ake kuti: “Ndifufuzireni mkazi waluso polankhula ndi mizimu,+ ndipo ine ndipita kukalankhula naye.” Pamenepo atumiki ake anamuuza kuti: “Ku Eni-dori alipo mkazi waluso polankhula ndi mizimu.”+ Salimo 83:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anawonongedwa ku Eni-dori.+Anasanduka manyowa a m’nthaka.+
7 Pamapeto pake, Sauli anauza atumiki ake kuti: “Ndifufuzireni mkazi waluso polankhula ndi mizimu,+ ndipo ine ndipita kukalankhula naye.” Pamenepo atumiki ake anamuuza kuti: “Ku Eni-dori alipo mkazi waluso polankhula ndi mizimu.”+