Yoswa 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a Yosefe analankhula ndi Yoswa kuti: “N’chifukwa chiyani mwatipatsa gawo limodzi lokha+ kuti likhale cholowa chathu, chikhalirecho tilipo anthu ochuluka popeza Yehova watidalitsa mpaka pano?”+
14 Ana a Yosefe analankhula ndi Yoswa kuti: “N’chifukwa chiyani mwatipatsa gawo limodzi lokha+ kuti likhale cholowa chathu, chikhalirecho tilipo anthu ochuluka popeza Yehova watidalitsa mpaka pano?”+