Yoswa 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Malirewo anapitirira mpaka ku Beti-hogila+ n’kukadutsa kumpoto kwa Beti-araba,+ n’kukafika kumwala wa Bohani,+ mwana wa Rubeni.
6 Malirewo anapitirira mpaka ku Beti-hogila+ n’kukadutsa kumpoto kwa Beti-araba,+ n’kukafika kumwala wa Bohani,+ mwana wa Rubeni.