Oweruza 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Benjamini anamva kuti ana a Isiraeli apita ku Mizipa.+ Pamenepo ana a Isiraeli anati: “Lankhulani, kodi chinthu choipachi chachitika bwanji?”+
3 Ana a Benjamini anamva kuti ana a Isiraeli apita ku Mizipa.+ Pamenepo ana a Isiraeli anati: “Lankhulani, kodi chinthu choipachi chachitika bwanji?”+