Yoswa 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ku Sefela+ kunali Esitaoli,+ Zora,+ Asina, Oweruza 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyi panali mwamuna wina wa ku Zora+ wa fuko la Dani,+ ndipo dzina lake anali Manowa.+ Mkazi wake anali wosabereka, moti analibe mwana.+ 2 Mbiri 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zora,+ Aijaloni+ ndi Heburoni.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri imene inali ku Yuda ndi ku Benjamini.
2 Pa nthawiyi panali mwamuna wina wa ku Zora+ wa fuko la Dani,+ ndipo dzina lake anali Manowa.+ Mkazi wake anali wosabereka, moti analibe mwana.+
10 Zora,+ Aijaloni+ ndi Heburoni.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri imene inali ku Yuda ndi ku Benjamini.