Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tembenukani ndi kulowera kudera lamapiri la Aamori+ ndi anthu oyandikana nawo onse okhala ku Araba,+ kudera lamapiri,+ ku Sefela, ku Negebu,+ m’mbali mwa nyanja,+ m’dziko la Akanani+ ndi ku Lebanoni+ mpaka kumtsinje waukulu wa Firate.+

  • Yoswa 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mafumu+ a kutsidya kwa Yorodano anamva zimene zinachitika. Amenewa anali mafumu a Ahiti,+ Aamori, Akanani,+ Aperezi,+ Ahivi ndi Ayebusi.+ Iwo anali kukhala kudera lamapiri, ndiponso ku Sefela, ndi m’mbali monse mwa Nyanja Yaikulu,+ komanso pafupi ndi Lebanoni.+ Mafumu onsewo atangomva zimene zinachitikazo,

  • Oweruza 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako ana a Yuda anatsika kukamenyana ndi Akanani okhala m’dera lamapiri, ku Negebu+ ndi ku Sefela.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena