Deuteronomo 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Udzadzilambulire njira yopita kumizindayo ndipo udzagawe dziko limene Yehova Mulungu wako wakupatsa kuti likhale lako. Dzikolo udzaligawe m’zigawo zitatu. Wopha munthu azithawira kumizinda imeneyo.+
3 Udzadzilambulire njira yopita kumizindayo ndipo udzagawe dziko limene Yehova Mulungu wako wakupatsa kuti likhale lako. Dzikolo udzaligawe m’zigawo zitatu. Wopha munthu azithawira kumizinda imeneyo.+