Ekisodo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo,+ udzautse chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.+ Yoswa 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+
2 “Mwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo,+ udzautse chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.+
18 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linasonkhana ku Silo,+ ndipo kumeneko anamangako chihema chokumanako,+ popeza anali atagonjetsa dziko lomwe linali pamaso pawo.+