Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 14:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Limeneli ndilo dziko limene ana a Isiraeli anatenga monga cholowa chawo m’dziko la Kanani.+ Wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mafuko a makolo a ana a Isiraeli, ndiwo anagawa dzikolo kuti likhale cholowa chawo.+

  • 1 Samueli 11:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iye anatenga ng’ombe ziwiri zamphongo n’kuziduladula. Kenako anatumiza amithenga kukapereka zigawo za ng’ombezo m’dziko lonse la Isiraeli+ ndipo anati: “Aliyense amene satsatira Sauli ndi Samueli, izi n’zimene zichitikire ng’ombe zake.”+ Anthu atamva mawu amenewa anagwidwa ndi mantha+ ochokera kwa Yehova,+ moti onse anapita mogwirizana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena