1 Samueli 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ anadziwa kuti Samueli ndiye anali wovomerezeka kukhala mneneri wa Yehova.+ 2 Samueli 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mfumu inauza Yowabu+ mkulu wa magulu ankhondo amene anali naye kuti: “Yendayenda m’mafuko onse a Isiraeli kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba.+ Ndipo amuna inu muwerenge anthu+ kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”+
20 Tsopano Aisiraeli onse kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba,+ anadziwa kuti Samueli ndiye anali wovomerezeka kukhala mneneri wa Yehova.+
2 Choncho mfumu inauza Yowabu+ mkulu wa magulu ankhondo amene anali naye kuti: “Yendayenda m’mafuko onse a Isiraeli kuchokera ku Dani mpaka ku Beere-seba.+ Ndipo amuna inu muwerenge anthu+ kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”+