Oweruza 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyankha mbuye wakeyo anati: “Tisapatukire mumzinda wa anthu achilendo+ amene si ana a Isiraeli. Tiyeni tipitirire ndi kukafika ku Gibeya.”+
12 Poyankha mbuye wakeyo anati: “Tisapatukire mumzinda wa anthu achilendo+ amene si ana a Isiraeli. Tiyeni tipitirire ndi kukafika ku Gibeya.”+