2 Samueli 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Davide anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, ndipereka ndithu Afilisitiwa m’manja mwako.”+
19 Ndiyeno Davide anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, ndipereka ndithu Afilisitiwa m’manja mwako.”+