Deuteronomo 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 muzipha ndithu anthu a mumzindawo ndi lupanga.+ Muziwononga+ ndi lupanga mzindawo ndi chilichonse chimene chili mmenemo, kuphatikizapo ziweto zake. Oweruza 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho amuna osankhidwa mwapadera a Isiraeli yense, okwana 10,000 anayandikira mzinda wa Gibeya, ndipo panaulika chinkhondo choopsa. Ana a Benjamini sanadziwe kuti tsoka+ latsala pang’ono kuwagwera.
15 muzipha ndithu anthu a mumzindawo ndi lupanga.+ Muziwononga+ ndi lupanga mzindawo ndi chilichonse chimene chili mmenemo, kuphatikizapo ziweto zake.
34 Choncho amuna osankhidwa mwapadera a Isiraeli yense, okwana 10,000 anayandikira mzinda wa Gibeya, ndipo panaulika chinkhondo choopsa. Ana a Benjamini sanadziwe kuti tsoka+ latsala pang’ono kuwagwera.