Levitiko 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musamalumbire zabodza m’dzina langa+ ndi kuipitsa dzina la Mulungu wanu. Ine ndine Yehova. Oweruza 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano amuna a Isiraeli analumbira ali ku Mizipa+ kuti: “Aliyense wa ife sadzapereka mwana wake wamkazi kuti akwatiwe ndi mwamuna wa fuko la Benjamini.”+ Salimo 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye sagwirizana ndi munthu aliyense wonyansa,+Koma anthu oopa Yehova amawalemekeza.+Akalumbira kuchita zinthu zimene kenako zakhala zoipa kwa iye, sasintha malingaliro ake.+ Mateyu 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+
21 Tsopano amuna a Isiraeli analumbira ali ku Mizipa+ kuti: “Aliyense wa ife sadzapereka mwana wake wamkazi kuti akwatiwe ndi mwamuna wa fuko la Benjamini.”+
4 Iye sagwirizana ndi munthu aliyense wonyansa,+Koma anthu oopa Yehova amawalemekeza.+Akalumbira kuchita zinthu zimene kenako zakhala zoipa kwa iye, sasintha malingaliro ake.+
33 “Komanso munamva kuti anthu akale anauzidwa kuti, ‘Usamalumbire+ koma osachita, m’malomwake uzikwaniritsa malonjezo ako kwa Yehova.’+