Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Apatuka mofulumira panjira imene ndawalamula kuyendamo.+ Iwo adzipangira fano la mwana wa ng’ombe lopangidwa ndi golide wosungunula. Akuligwadira ndi kupereka nsembe kwa fanolo, ndipo akunena kuti, ‘Aisiraeli inu, uyu ndiye Mulungu wanu amene anakutsogolerani potuluka m’dziko la Iguputo.’”+

  • Deuteronomo 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo Yehova anandiuza kuti, ‘Nyamuka, tsika mofulumira m’phiri muno, chifukwa anthu ako amene unawatulutsa ku Iguputo achita zinthu zowawonongetsa.+ Apatuka mofulumira panjira imene ndinawalamula kuyendamo. Adzipangira chifaniziro chopangidwa ndi chitsulo chosungunula.’+

  • Oweruza 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo anthuwo anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse a Yoswa ndi masiku onse a akulu amene anapitiriza kukhala ndi moyo Yoswa atamwalira, akulu amene anaona ntchito zonse zazikulu zimene Yehova anachitira Isiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena