Deuteronomo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (Asidoni anali kutcha phiri la Herimoni kuti Sirioni,+ pamene Aamori anali kulitcha kuti Seniri.)+ Yoswa 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 dziko la Agebala+ ndiponso dziko lonse la Lebanoni, kotulukira dzuwa, kuyambira ku Baala-gadi+ m’munsi mwa phiri la Herimoni mpaka kumalire ndi Hamati.+
5 dziko la Agebala+ ndiponso dziko lonse la Lebanoni, kotulukira dzuwa, kuyambira ku Baala-gadi+ m’munsi mwa phiri la Herimoni mpaka kumalire ndi Hamati.+