Oweruza 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Baraki anathamangitsa+ magaleta ankhondowo+ ndi gulu lonselo mpaka ku Haroseti-ha-goimu, moti gulu lonse la Sisera linaphedwa ndi lupanga. Sipanatsale ndi mmodzi yemwe.+
16 Baraki anathamangitsa+ magaleta ankhondowo+ ndi gulu lonselo mpaka ku Haroseti-ha-goimu, moti gulu lonse la Sisera linaphedwa ndi lupanga. Sipanatsale ndi mmodzi yemwe.+