Yesaya 43:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amatsogolera magaleta ankhondo ndi mahatchi, komanso gulu lankhondo ndi asilikali amphamvu pa nthawi imodzi.+ Iye wanena kuti: “Iwo adzagona pansi,+ sadzadzuka+ ndipo adzatha.+ Adzazimitsidwa ngati chingwe cha nyale.”+
17 Amatsogolera magaleta ankhondo ndi mahatchi, komanso gulu lankhondo ndi asilikali amphamvu pa nthawi imodzi.+ Iye wanena kuti: “Iwo adzagona pansi,+ sadzadzuka+ ndipo adzatha.+ Adzazimitsidwa ngati chingwe cha nyale.”+