Oweruza 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Sisera+ anathawa wapansi kupita kuhema wa Yaeli,+ mkazi wa Hiberi Mkeni,+ pakuti panali mtendere pakati pa Yabini mfumu ya Hazori+ ndi nyumba ya Hiberi Mkeni.
17 Koma Sisera+ anathawa wapansi kupita kuhema wa Yaeli,+ mkazi wa Hiberi Mkeni,+ pakuti panali mtendere pakati pa Yabini mfumu ya Hazori+ ndi nyumba ya Hiberi Mkeni.