Oweruza 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku a Samagara+ mwana wa Anati,M’masiku a Yaeli,+ m’njira munalibe odutsamo,Ndipo oyenda m’misewu anayamba kuyenda njira zolambalala.+ Oweruza 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yaeli,+ mkazi wa Hiberi Mkeni,+ akhale wodalitsika pakati pa akazi onse,Akhale wodalitsika pakati pa akazi onse okhala m’mahema.+
6 M’masiku a Samagara+ mwana wa Anati,M’masiku a Yaeli,+ m’njira munalibe odutsamo,Ndipo oyenda m’misewu anayamba kuyenda njira zolambalala.+
24 Yaeli,+ mkazi wa Hiberi Mkeni,+ akhale wodalitsika pakati pa akazi onse,Akhale wodalitsika pakati pa akazi onse okhala m’mahema.+