Deuteronomo 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma musaphe akazi, ana aang’ono,+ ziweto+ ndi chilichonse chopezeka mumzindawo. Muzifunkha+ zinthu zonse za mumzindawo ndipo muzidya zimene mwafunkha kwa adani anu amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+ Deuteronomo 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndipo pakati pa anthu ogwidwawo waonapo mkazi wamaonekedwe okongola ndipo wakopeka+ naye ndi kum’tenga kuti akhale mkazi wako,
14 Koma musaphe akazi, ana aang’ono,+ ziweto+ ndi chilichonse chopezeka mumzindawo. Muzifunkha+ zinthu zonse za mumzindawo ndipo muzidya zimene mwafunkha kwa adani anu amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
11 ndipo pakati pa anthu ogwidwawo waonapo mkazi wamaonekedwe okongola ndipo wakopeka+ naye ndi kum’tenga kuti akhale mkazi wako,