Genesis 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+ Numeri 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Amuna inu, athireni nkhondo Amidiyani, ndipo muwakanthe,+ Oweruza 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amidiyaniwo anayamba kusautsa Aisiraeli.+ Chifukwa cha kusautsidwa ndi Amidiyani kumeneku, ana a Isiraeli anadzikonzera malo apansi osungiramo zinthu m’mapiri. Anadzikonzeranso mapanga ndi malo ena ovuta kufikako kuti azithawirako.+
2 M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+
2 Amidiyaniwo anayamba kusautsa Aisiraeli.+ Chifukwa cha kusautsidwa ndi Amidiyani kumeneku, ana a Isiraeli anadzikonzera malo apansi osungiramo zinthu m’mapiri. Anadzikonzeranso mapanga ndi malo ena ovuta kufikako kuti azithawirako.+