Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo.

  • Ekisodo 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Patapita nthawi, Farao anaimva nkhaniyi ndipo anafuna kupha Mose.+ Koma Mose anam’thawa+ Farao ndipo anapita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pachitsime.

  • Numeri 22:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo Amowabu anakalankhula ndi akuluakulu a ku Midiyani,+ kuti: “Chikhamuchi chidzamwetula malo athu onse monga ng’ombe yomwetula msipu kubusa.”

      Pa nthawi imeneyo, Balaki+ mwana wa Zipori ndiye anali mfumu ya Mowabu.

  • Numeri 31:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Uwabwezere+ Amidiyani+ pa zimene anachitira ana a Isiraeli. Pambuyo pake udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.”+

  • Oweruza 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Amidiyaniwo anayamba kusautsa Aisiraeli.+ Chifukwa cha kusautsidwa ndi Amidiyani kumeneku, ana a Isiraeli anadzikonzera malo apansi osungiramo zinthu m’mapiri. Anadzikonzeranso mapanga ndi malo ena ovuta kufikako kuti azithawirako.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena