Oweruza 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Yowasi anatcha Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala*+ pa tsiku limenelo, ndipo anati: “Baala adziweruzire yekha mlandu, chifukwa winawake wagwetsa guwa lake lansembe.”+ 1 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+
32 Choncho Yowasi anatcha Gidiyoni dzina lakuti Yerubaala*+ pa tsiku limenelo, ndipo anati: “Baala adziweruzire yekha mlandu, chifukwa winawake wagwetsa guwa lake lansembe.”+
11 Pamenepo Yehova anatumiza Yerubaala,+ Bedani, Yefita+ ndi Samueli+ ndipo anakulanditsani m’manja mwa adani anu onse okuzungulirani, kuti mukhale popanda chokuopsani.+