Salimo 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndikakumbukira inu ndili pabedi langa,+Pa nthawi za ulonda wa usiku* ndimasinkhasinkha za inu.+ Luka 12:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo ndi odala ndithu ngati atawapeza akudikirabe ngakhale atafika pa ulonda wachiwiri kapenanso wachitatu!*+
38 Iwo ndi odala ndithu ngati atawapeza akudikirabe ngakhale atafika pa ulonda wachiwiri kapenanso wachitatu!*+