1 Samueli 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nawonso amuna onse a Isiraeli amene anali atabisala+ m’dera lamapiri la Efuraimu anamva kuti Afilisiti athawa, choncho Aisiraeliwo anayamba kuthamangitsa Afilisitiwo ndi kuwathira nkhondo.
22 Nawonso amuna onse a Isiraeli amene anali atabisala+ m’dera lamapiri la Efuraimu anamva kuti Afilisiti athawa, choncho Aisiraeliwo anayamba kuthamangitsa Afilisitiwo ndi kuwathira nkhondo.