Yoswa 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuchokera ku hafu ya fuko la Manase, anawapatsa Taanaki+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Gati-rimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Inalipo mizinda iwiri. Oweruza 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Pamenepo mafumu a Kanani anamenya nkhondo,+Anamenya nkhondo ku Taanaki,+ pafupi ndi madzi a ku Megido.+Iwo sanapezepo phindu la siliva.+
25 Kuchokera ku hafu ya fuko la Manase, anawapatsa Taanaki+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Gati-rimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Inalipo mizinda iwiri.
19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.Pamenepo mafumu a Kanani anamenya nkhondo,+Anamenya nkhondo ku Taanaki,+ pafupi ndi madzi a ku Megido.+Iwo sanapezepo phindu la siliva.+