Yoswa 12:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mfumu ya Dori kumapiri a Dori,+ imodzi. Mfumu ya Goimu ku Giligala, imodzi. Yoswa 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Manase analephera kulanda mizindayi,+ moti Akanani anakakamira kukhalabe m’derali.+
23 Mfumu ya Dori kumapiri a Dori,+ imodzi. Mfumu ya Goimu ku Giligala, imodzi. Yoswa 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Manase analephera kulanda mizindayi,+ moti Akanani anakakamira kukhalabe m’derali.+