Genesis 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero Sara anayamba kuuza Abulahamu kuti: “Thamangitsani kapolo wamkaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, chifukwa mwana wa kapolo ameneyu sadzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wanga Isaki.”+ Deuteronomo 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Mwamuna akakhala ndi akazi awiri, wina wokondedwa ndi wina wosakondedwa, ndipo onse awiri, wokondedwa ndi wosakondedwayo, abereka ana aamuna ndi mwamunayo, koma mwana wa mkazi wosakondedwayo ndiye woyamba kubadwa,+
10 Chotero Sara anayamba kuuza Abulahamu kuti: “Thamangitsani kapolo wamkaziyu pamodzi ndi mwana wakeyu pano, chifukwa mwana wa kapolo ameneyu sadzakhala wolandira cholowa pamodzi ndi mwana wanga Isaki.”+
15 “Mwamuna akakhala ndi akazi awiri, wina wokondedwa ndi wina wosakondedwa, ndipo onse awiri, wokondedwa ndi wosakondedwayo, abereka ana aamuna ndi mwamunayo, koma mwana wa mkazi wosakondedwayo ndiye woyamba kubadwa,+