Genesis 29:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno Yakobo anagonanso ndi Rakele, ndipo anam’konda kwambiri Rakele kuposa Leya.+ Motero anagwiriranso ntchito Labani zaka zina 7.+ Genesis 29:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Leya anakhalanso ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wandimvera+ kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamutcha Simiyoni.*+ 1 Samueli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno tsiku lina Elikana anali kupereka nsembe, ndipo anapereka magawo a nsembeyo kwa mkazi wake Penina ndi kwa ana ake onse aamuna ndi aakazi,+
30 Ndiyeno Yakobo anagonanso ndi Rakele, ndipo anam’konda kwambiri Rakele kuposa Leya.+ Motero anagwiriranso ntchito Labani zaka zina 7.+
33 Leya anakhalanso ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Yehova wandipatsa mwana wina chifukwa wandimvera+ kuti sindikukondedwa kwenikweni.” Choncho mwanayo anamutcha Simiyoni.*+
4 Ndiyeno tsiku lina Elikana anali kupereka nsembe, ndipo anapereka magawo a nsembeyo kwa mkazi wake Penina ndi kwa ana ake onse aamuna ndi aakazi,+