Genesis 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Abele nayenso anabweretsa ana oyamba+ a nkhosa zake n’kuwapereka nsembe, ndipo anaperekanso nsembe mafuta a nkhosazo.+ Yehova anakondwera ndi Abele ndipo analandira nsembe yake,+ Oweruza 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Poyankha, mngelo wa Yehova anauza Manowa kuti: “Ngakhale mundichedwetse sindidya mkate wanu. Koma ngati mungathe kupereka kwa Yehova nsembe yopsereza,+ perekani.” Manowa ananena zimenezi chifukwa sanadziwe kuti anali mngelo wa Yehova.
4 Abele nayenso anabweretsa ana oyamba+ a nkhosa zake n’kuwapereka nsembe, ndipo anaperekanso nsembe mafuta a nkhosazo.+ Yehova anakondwera ndi Abele ndipo analandira nsembe yake,+
16 Poyankha, mngelo wa Yehova anauza Manowa kuti: “Ngakhale mundichedwetse sindidya mkate wanu. Koma ngati mungathe kupereka kwa Yehova nsembe yopsereza,+ perekani.” Manowa ananena zimenezi chifukwa sanadziwe kuti anali mngelo wa Yehova.