Oweruza 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anapita kukauza bambo ndi mayi ake kuti: “Ine ndaona mkazi ku Timuna mwa ana aakazi a Afilisiti, choncho mukam’tenge kuti akhale mkazi wanga.”+
2 Kenako anapita kukauza bambo ndi mayi ake kuti: “Ine ndaona mkazi ku Timuna mwa ana aakazi a Afilisiti, choncho mukam’tenge kuti akhale mkazi wanga.”+