Oweruza 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Patapita nthawi, Samisoni anabwerera kwa mkaziyo kuti akam’tenge ndi kupita naye kwawo.+ Ali m’njira, anapatuka kuti aone mkango umene anapha uja. Atafika pamene anaphera mkango paja anapeza kuti m’thupi la mkango wakufa uja muli njuchi ndi uchi.+
8 Patapita nthawi, Samisoni anabwerera kwa mkaziyo kuti akam’tenge ndi kupita naye kwawo.+ Ali m’njira, anapatuka kuti aone mkango umene anapha uja. Atafika pamene anaphera mkango paja anapeza kuti m’thupi la mkango wakufa uja muli njuchi ndi uchi.+