Oweruza 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Delila anauza Samisoni kuti: “Kodi ulibe manyazi kundiuza kuti, ‘Ndimakukonda,’+ pamene mtima wako suli pa ine? Katatu konse tsopano wakhala ukundipusitsa, ndipo sunandiuze chinsinsi cha mphamvu zako zazikuluzi.”+
15 Ndiyeno Delila anauza Samisoni kuti: “Kodi ulibe manyazi kundiuza kuti, ‘Ndimakukonda,’+ pamene mtima wako suli pa ine? Katatu konse tsopano wakhala ukundipusitsa, ndipo sunandiuze chinsinsi cha mphamvu zako zazikuluzi.”+