Oweruza 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho iye anati:“M’chinthu chodya zinzake+ munatuluka chakudya,Ndipo m’chinthu champhamvu munatuluka zinthu zokoma.”+ Koma anzake a mkwatiwo analephera kumasulira mwambiwo kwa masiku atatu.
14 Choncho iye anati:“M’chinthu chodya zinzake+ munatuluka chakudya,Ndipo m’chinthu champhamvu munatuluka zinthu zokoma.”+ Koma anzake a mkwatiwo analephera kumasulira mwambiwo kwa masiku atatu.