Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 24:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Munthu aliyense amene wakantha ndi kupheratu mnzake, nayenso aziphedwa ndithu.+

  • Oweruza 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zitatero, Adoni-bezeki anati: “Panali mafumu 70 odulidwa zala zamanthu za m’manja ndi zala zazikulu za kumapazi, amene anali kutola chakudya pansi pa tebulo langa. Mulungu wandibwezera zimene ndinachita.”+ Kenako anam’tengera ku Yerusalemu+ kumene anakafera.

  • Oweruza 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo Samisoni anawauza kuti: “Pa zimene mwachitazi, ine sindingachitire mwina koma kukubwezerani,+ ndipo ndikatero ndisiyira pamenepo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena