Genesis 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Mulungu anamutsegula maso Hagara, moti anaona chitsime cha madzi.+ Chotero iye anapita pachitsimecho n’kutungira madziwo m’thumba lachikopa lija, n’kumupatsa mnyamatayo kuti amwe. Ekisodo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli, Mateyu 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yesu anawayang’anitsitsa n’kunena kuti: “Kwa anthu zimenezi n’zosathekadi, koma zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu.”+
19 Ndiyeno Mulungu anamutsegula maso Hagara, moti anaona chitsime cha madzi.+ Chotero iye anapita pachitsimecho n’kutungira madziwo m’thumba lachikopa lija, n’kumupatsa mnyamatayo kuti amwe.
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli,
26 Yesu anawayang’anitsitsa n’kunena kuti: “Kwa anthu zimenezi n’zosathekadi, koma zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu.”+