Salimo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wosautsikayu anaitana ndipo Yehova anamva.+Anamupulumutsa m’masautso ake onse.+ Salimo 120:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 120 Ndinafuulira Yehova m’masautso anga,+Ndipo iye anandiyankha.+