Genesis 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+ Genesis 24:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Ndiyeno iwo anayamba kudalitsa Rabeka kuti: “Iwe mlongo wathu, ukakhale mayi wa anthu masauzande kuchulukitsa ndi masauzande 10, ndipo mbewu yako ikalande mizinda ya adani awo.”+
17 ndidzakudalitsa ndithu. Ndiponso ndidzachulukitsadi mbewu yako ngati nyenyezi zakumwamba, monganso mchenga wa m’mphepete mwa nyanja.+ Komanso mbewu yako idzalanda chipata* cha adani ake.+
60 Ndiyeno iwo anayamba kudalitsa Rabeka kuti: “Iwe mlongo wathu, ukakhale mayi wa anthu masauzande kuchulukitsa ndi masauzande 10, ndipo mbewu yako ikalande mizinda ya adani awo.”+