Deuteronomo 32:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+ Oweruza 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+
27 Ngati ndikanati sindikuopa kusautsidwa ndi mdani,+Kuti adani awo angamve molakwa,+Kutinso anganene kuti: “Dzanja lathu lapambana,+Ndipo si Yehova amene wachita zonsezi.”+
5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+