Genesis 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Mulungu anamva mawu a mnyamatayo,+ ndipo mngelo wa Mulungu analankhula ndi Hagara kuchokera kumwamba+ kuti: “Kodi watani Hagara? Usaope, Mulungu wamva mawu a mnyamatayo pomwe wagonapo. 2 Samueli 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu inamufunsa kuti: “Kodi chavuta ndi chiyani?” Mkaziyo anayankha kuti: “Ine ndine mkazi wamasiye,+ pakuti mwamuna wanga anamwalira. 2 Mafumu 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno mfumuyo inam’funsa kuti: “Vuto lako ndi lotani?” Mayiyo anayankha kuti: “Mayi uyu anandiuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye lero, ndipo mwana wanga timudya mawa.’+
17 Pamenepo Mulungu anamva mawu a mnyamatayo,+ ndipo mngelo wa Mulungu analankhula ndi Hagara kuchokera kumwamba+ kuti: “Kodi watani Hagara? Usaope, Mulungu wamva mawu a mnyamatayo pomwe wagonapo.
5 Ndiyeno mfumu inamufunsa kuti: “Kodi chavuta ndi chiyani?” Mkaziyo anayankha kuti: “Ine ndine mkazi wamasiye,+ pakuti mwamuna wanga anamwalira.
28 Ndiyeno mfumuyo inam’funsa kuti: “Vuto lako ndi lotani?” Mayiyo anayankha kuti: “Mayi uyu anandiuza kuti, ‘Bweretsa mwana wako timudye lero, ndipo mwana wanga timudya mawa.’+