Luka 1:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Anthu oyandikana naye ndi abale ake anamva kuti Yehova anam’chitira chifundo chachikulu,+ ndipo anayamba kukondwera+ naye pamodzi. Aroma 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sangalalani ndi anthu amene akusangalala.+ Lirani ndi anthu amene akulira.
58 Anthu oyandikana naye ndi abale ake anamva kuti Yehova anam’chitira chifundo chachikulu,+ ndipo anayamba kukondwera+ naye pamodzi.