Oweruza 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo anthu a ku Gaza anauzidwa kuti: “Samisoni wabwera, ali kuno.” Choncho anam’zungulira+ ndi kum’bisalira usiku wonse kuchipata cha mzindawo.+ Iwo anakhala chete usiku wonse, n’kumanena mumtima mwawo kuti: “Kukangocha timuphe.”+
2 Pamenepo anthu a ku Gaza anauzidwa kuti: “Samisoni wabwera, ali kuno.” Choncho anam’zungulira+ ndi kum’bisalira usiku wonse kuchipata cha mzindawo.+ Iwo anakhala chete usiku wonse, n’kumanena mumtima mwawo kuti: “Kukangocha timuphe.”+