1 Samueli 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mkaziyo ataona “Samueli”*+ anayamba kulira mofuula kwambiri. Kenako mkaziyo anauza Sauli kuti: “N’chifukwa chiyani mwandipusitsa, pamene inuyo ndinu Sauli amene?”
12 Mkaziyo ataona “Samueli”*+ anayamba kulira mofuula kwambiri. Kenako mkaziyo anauza Sauli kuti: “N’chifukwa chiyani mwandipusitsa, pamene inuyo ndinu Sauli amene?”