1 Samueli 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo Hana anati: “Pepani mbuyanga! Pali moyo wanu+ mbuyanga, ine ndine mkazi amene ndinaima ndi inu pamalo ano n’kupemphera kwa Yehova.+ 1 Samueli 17:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Sauli ataona Davide akupita kukakumana ndi Mfilisiti uja, anafunsa Abineri,+ mkulu wa asilikali, kuti: “Kodi ameneyu ndi mwana+ wa ndani,+ Abineri?” Poyankha Abineri anati: “Ndikulumbira pali moyo wanu mfumu, ine sindikudziwa ngakhale pang’ono!”
26 Pamenepo Hana anati: “Pepani mbuyanga! Pali moyo wanu+ mbuyanga, ine ndine mkazi amene ndinaima ndi inu pamalo ano n’kupemphera kwa Yehova.+
55 Sauli ataona Davide akupita kukakumana ndi Mfilisiti uja, anafunsa Abineri,+ mkulu wa asilikali, kuti: “Kodi ameneyu ndi mwana+ wa ndani,+ Abineri?” Poyankha Abineri anati: “Ndikulumbira pali moyo wanu mfumu, ine sindikudziwa ngakhale pang’ono!”