1 Samueli 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Yonatani analumbiranso kwa Davide chifukwa chakuti anali kum’konda kwambiri. Pakuti Yonatani anali kukonda Davide monga mmene anali kudzikondera iye mwini.+ 1 Samueli 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova akhale mboni yathu mpaka kalekale,+ pa mawu awa amene tauzana+ ine ndi iwe.”
17 Choncho Yonatani analumbiranso kwa Davide chifukwa chakuti anali kum’konda kwambiri. Pakuti Yonatani anali kukonda Davide monga mmene anali kudzikondera iye mwini.+