Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Sarai ataona zimenezi anauza Abulamu kuti: “Mlandu wa chipongwe chikundichitikirachi ukhale pa inu. Ine ndinapereka kapolo wanga kwa inu kuti akhale mkazi wanu, koma iye poona kuti watenga pakati wayamba kundichitira chipongwe. Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu.”+

  • 1 Samueli 20:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Pamenepo Yonatani anauza Davide kuti: “Pita mu mtendere,+ pakuti tonse awiri talumbira+ m’dzina la Yehova kuti, ‘Yehova akhale pakati pa iwe ndi ine, ndi pakati pa ana ako ndi ana anga mpaka kalekale.’”+

      Chotero Davide ananyamuka ndi kupita, koma Yonatani anabwerera kumzinda.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena