Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 6:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Yehova akuyang’aneni mokondwera+ ndipo akupatseni mtendere.”’+

  • 1 Samueli 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo Eli anamuyankha kuti: “Pita mu mtendere,+ ndipo Mulungu wa Isiraeli akupatse zimene wam’pempha.”+

  • Luka 7:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Koma iye anauza mayiyo kuti: “Chikhulupiriro chako chakupulumutsa.+ Pita mu mtendere.”+

  • Machitidwe 16:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Choncho woyang’anira ndende uja anauza Paulo uthengawo, kuti: “Akuluakulu a boma atumiza anthu kudzanena kuti awirinu mumasulidwe. Choncho tulukani tsopano, ndipo mupite mu mtendere.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena